Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+

  • Oweruza 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Kalekale mitengo inafuna kudzoza mfumu yawo. Pamenepo mitengoyo inauza mtengo wa maolivi+ kuti, ‘Iwe ukhale mfumu yathu.’+

  • 1 Samueli 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma zimenezi zinamuipira Samueli, chifukwa iwo anati: “Utipatse mfumu yoti izitiweruza.” Pamenepo Samueli anayamba kupemphera kwa Yehova.+

  • 1 Samueli 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mutaona kuti mfumu ya ana a Amoni, Nahasi,+ yabwera kudzamenyana nanu, munayamba kundiuza kuti, ‘Ife tikufuna kuti mfumu izitilamulira!’+ ngakhale kuti Yehova Mulungu wanu ndiye Mfumu yanu.+

  • Hoseya 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Tsopano mfumu yako ili kuti, kuti ikupulumutse m’mizinda yako yonse.+ Oweruza ako ali kuti amene unawauza kuti, ‘Ndipatseni mfumu ndi akalonga’?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena