1 Samueli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.” 1 Samueli 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma anthuwo anakana kumvera mawu a Samueli+ ndipo anati: “Ife tikufuna kuti mfumu izitilamulira.
5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”