Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+

  • 1 Samueli 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano mfumu imene mwasankha ndi imeneyi, mfumu imene mwapempha.+ Ndipotu Yehova wakuikiranidi mfumu+ yoti izikulamulirani.

  • Hoseya 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Tsopano mfumu yako ili kuti, kuti ikupulumutse m’mizinda yako yonse.+ Oweruza ako ali kuti amene unawauza kuti, ‘Ndipatseni mfumu ndi akalonga’?+

  • Machitidwe 13:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma kuchokera pamenepo anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Chotero Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena