1 Samueli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini malinga ndi mabanja awo, ndipo banja la Amatiri linasankhidwa.+ Pamapeto pake, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Choncho anayamba kum’funafuna, koma sanam’peze. 1 Samueli 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anthu onse anapita ku Giligala ndipo analonga Sauli kukhala mfumu pamaso pa Yehova ku Giligalako. Kenako anapereka nsembe zachiyanjano pamaso pa Yehova+ kumeneko, ndipo Sauli pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli anali osangalala kwambiri.+
21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini malinga ndi mabanja awo, ndipo banja la Amatiri linasankhidwa.+ Pamapeto pake, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Choncho anayamba kum’funafuna, koma sanam’peze.
15 Choncho anthu onse anapita ku Giligala ndipo analonga Sauli kukhala mfumu pamaso pa Yehova ku Giligalako. Kenako anapereka nsembe zachiyanjano pamaso pa Yehova+ kumeneko, ndipo Sauli pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli anali osangalala kwambiri.+