Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Tsopano lamulo la nsembe yachiyanjano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova lili motere: 1 Samueli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”
8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”