1 Samueli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako ukatsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Ukandidikire masiku 7 mpaka nditabwera ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”
8 Kenako ukatsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Ukandidikire masiku 7 mpaka nditabwera ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”