1 Samueli 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Sauli anati: “Bweretsani kuno nsembe yopsereza ndi nsembe zachiyanjano.” Pamenepo iye anapereka nsembe yopserezayo.+
9 Kenako Sauli anati: “Bweretsani kuno nsembe yopsereza ndi nsembe zachiyanjano.” Pamenepo iye anapereka nsembe yopserezayo.+