Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+ Levitiko 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Munthu amene wadya nyama ya nsembe yachiyanjano, imene ndi ya Yehova, pamene munthuyo ali wodetsedwa, aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+ Levitiko 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake+ kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ng’ombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse. 1 Akorinto 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?
3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+
20 “‘Munthu amene wadya nyama ya nsembe yachiyanjano, imene ndi ya Yehova, pamene munthuyo ali wodetsedwa, aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+
21 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake+ kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ng’ombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.
16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?