-
Levitiko 15:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndipo adzakhala wodetsedwa ndi nthendayo ngati akukha kumaliseche, kapena ngati maliseche ake atsekeka ndi zimene zikukhazo. Zikatere azikhala wodetsedwa.
-