Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Koma ngati mukupereka ng’ombe yamphongo monga nsembe yopsereza,+ kapena monga nsembe yochitira lonjezo lapadera,+ kapenanso monga nsembe zachiyanjano kwa Yehova,+

  • Deuteronomo 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Ukapereka lonjezo kwa Yehova+ Mulungu wako usachedwe kulikwaniritsa kuopera kuti ungachimwe,+ chifukwa Yehova Mulungu wako adzafuna ndithu kuti ukwaniritse chimene walonjezacho.+

  • Salimo 50:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pereka nsembe zoyamikira kwa Mulungu,+

      Ndipo pereka kwa Wam’mwambamwamba zimene walonjeza.+

  • Salimo 61:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Choncho ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu mpaka muyaya,+

      Kuti ndikwaniritse malonjezo anga tsiku ndi tsiku.+

  • Mlaliki 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena