Levitiko 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ngati akupereka lonjezo+ monga nsembe yake kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo angathenso kudya imene yatsala pa tsiku lotsatira.
16 “‘Ngati akupereka lonjezo+ monga nsembe yake kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo angathenso kudya imene yatsala pa tsiku lotsatira.