Mlaliki 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+ Aroma 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 osazindikira,+ osasunga mapangano,+ opanda chikondi chachibadwa+ ndiponso opanda chifundo.+ Yakobo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero, ngati munthu akudziwa kuchita chabwino koma sakuchichita,+ akuchimwa.+
6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+