Salimo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+Ndi kuti aiyandikire.”+ Aroma 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chakuti, ngakhale anam’dziwa Mulungu, iwo sanam’patse ulemerero monga Mulungu kapena kumuyamikira.+ M’malomwake anayamba kulingalira zinthu zopanda pake+ ndipo mtima wawo wopusawo unachita mdima.+
9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+Ndi kuti aiyandikire.”+
21 Chifukwa chakuti, ngakhale anam’dziwa Mulungu, iwo sanam’patse ulemerero monga Mulungu kapena kumuyamikira.+ M’malomwake anayamba kulingalira zinthu zopanda pake+ ndipo mtima wawo wopusawo unachita mdima.+