Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+ Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Salimo 147:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amauza Yakobo mawu ake,+Ndipo amauza Isiraeli malangizo+ ake ndi zigamulo zake.+
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+
23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+