Salimo 78:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu anaika chikumbutso pakati pa ana a Yakobo,+Iye anaika chilamulo mu Isiraeli,+Zinthu zimene analamula makolo athu,+Kuti auze ana awo.+ Salimo 147:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amauza Yakobo mawu ake,+Ndipo amauza Isiraeli malangizo+ ake ndi zigamulo zake.+
5 Mulungu anaika chikumbutso pakati pa ana a Yakobo,+Iye anaika chilamulo mu Isiraeli,+Zinthu zimene analamula makolo athu,+Kuti auze ana awo.+ Salimo 147:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amauza Yakobo mawu ake,+Ndipo amauza Isiraeli malangizo+ ake ndi zigamulo zake.+