Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+ Deuteronomo 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma iwe ima pompano, ndipo ndikuuza malamulo onse, malangizo ndi zigamulo zimene uyenera kuwaphunzitsa+ kuti azikazitsatira m’dziko limene ndikuwapatsa kukhala lawo.’ Malaki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+
31 Koma iwe ima pompano, ndipo ndikuuza malamulo onse, malangizo ndi zigamulo zimene uyenera kuwaphunzitsa+ kuti azikazitsatira m’dziko limene ndikuwapatsa kukhala lawo.’
4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+