Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo, Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwachuluka padziko lapansi, ndipo malingaliro+ onse a m’mitima ya anthu anali oipa okhaokha nthawi zonse.+

  • Mateyu 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma Yesu, podziwa zimene iwo anali kuganiza,+ ananena kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zinthu zoipa m’mitima mwanu?+

  • Mateyu 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti anthu awa aumitsa mtima wawo, ndipo amva ndi makutu awo koma osalabadira. Atseka maso awo kuti asaone ndi maso awo ndi kumva ndi makutu awo ndi kuzindikira tanthauzo lake m’mitima yawo n’kutembenuka, kuti ine ndiwachiritse.’+

  • Luka 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma Yesu, pozindikira zimene anali kuganiza anawayankha kuti: “Kodi mukuganiza chiyani m’mitima mwanu?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena