Mateyu 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Samalani anthu inu kuti musanyoze mmodzi wa tianati, chifukwa ndikukutsimikizirani kuti angelo awo+ kumwamba amaona nkhope ya Atate wanga wakumwamba nthawi zonse.+ Luka 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Zekariya anafunsa mngeloyo kuti: “Nditsimikiza bwanji zimenezi? Inetu ndine wokalamba,+ mkazi wanganso zaka zake n’zambiri.”
10 Samalani anthu inu kuti musanyoze mmodzi wa tianati, chifukwa ndikukutsimikizirani kuti angelo awo+ kumwamba amaona nkhope ya Atate wanga wakumwamba nthawi zonse.+
18 Ndiyeno Zekariya anafunsa mngeloyo kuti: “Nditsimikiza bwanji zimenezi? Inetu ndine wokalamba,+ mkazi wanganso zaka zake n’zambiri.”