Genesis 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abulahamu atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi, n’kuyamba kuseka mumtima mwake+ kuti: “Kodi mwamuna wa zaka 100 angabereke mwana zoona? Komanso Sara mkazi wa zaka 90, zoona angakhale ndi mwana?”+ Genesis 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abulahamu ndi Sara anali okalamba ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Sara anali atasiya kusamba.+ Aroma 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+
17 Abulahamu atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi, n’kuyamba kuseka mumtima mwake+ kuti: “Kodi mwamuna wa zaka 100 angabereke mwana zoona? Komanso Sara mkazi wa zaka 90, zoona angakhale ndi mwana?”+
19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+