Genesis 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Sara anayamba kuseka mumtima mwake+ kwinaku akunena kuti: “Kodi mmene ndatheramu, zoona ndingakhaledi ndi chisangalalo chimenechi, komanso ndi mmene mbuyanga wakalambiramu?”+ Genesis 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Sara anati: “Mulungu wandipatsa chifukwa chosangalalira. Tsopano aliyense akamva zimenezi asangalala nane.”*+ Luka 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mariya anasunga mawu onsewa ndi kuganizira tanthauzo la zimenezi mumtima mwake.+
12 Chotero Sara anayamba kuseka mumtima mwake+ kwinaku akunena kuti: “Kodi mmene ndatheramu, zoona ndingakhaledi ndi chisangalalo chimenechi, komanso ndi mmene mbuyanga wakalambiramu?”+
6 Ndiyeno Sara anati: “Mulungu wandipatsa chifukwa chosangalalira. Tsopano aliyense akamva zimenezi asangalala nane.”*+