Genesis 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abale akewo anachita naye kaduka,+ koma bambo ake anasunga mawuwo.+ Luka 1:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Mwakuti onse amene anamva anazisunga m’mitima mwawo ndi kuzisinkhasinkha.+ Iwo anali kunena kuti: “Kodi mwana ameneyu adzakhala wotani kwenikweni?” Pakuti dzanja+ la Yehova linalidi pa iye. Luka 2:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo ananyamuka nawo limodzi kubwerera ku Nazareti, ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+
66 Mwakuti onse amene anamva anazisunga m’mitima mwawo ndi kuzisinkhasinkha.+ Iwo anali kunena kuti: “Kodi mwana ameneyu adzakhala wotani kwenikweni?” Pakuti dzanja+ la Yehova linalidi pa iye.
51 Pamenepo ananyamuka nawo limodzi kubwerera ku Nazareti, ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+