Luka 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mariya anasunga mawu onsewa ndi kuganizira tanthauzo la zimenezi mumtima mwake.+