Levitiko 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Ngati mkazi akukha ndipo zimene akukhazo ndi magazi,+ azikhala masiku 7 ali wodetsedwa+ chifukwa cha kusamba+ kwakeko, ndipo aliyense womukhudza azikhala wodetsedwa kufikira madzulo. Aroma 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+
19 “‘Ngati mkazi akukha ndipo zimene akukhazo ndi magazi,+ azikhala masiku 7 ali wodetsedwa+ chifukwa cha kusamba+ kwakeko, ndipo aliyense womukhudza azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.
19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+