Levitiko 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Mwamuna akagona ndi mkazi amene ali pa nyengo ya kusamba, onse awiri sanalemekeze magazi ake.+ Choncho onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.
18 “‘Mwamuna akagona ndi mkazi amene ali pa nyengo ya kusamba, onse awiri sanalemekeze magazi ake.+ Choncho onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.