Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mkazi akatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira akamasamba.+

  • Levitiko 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘Akabereka mwana wamkazi, azikhala wodetsedwa kwa masiku 14. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira akamasamba. Kwa masiku enanso 66 azikhala panyumba kuti ayeretsedwe ku magazi ake.

  • Levitiko 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Bedi lililonse limene angagonepo pa tsiku lililonse mwa masiku amene akukha magaziwo, lizikhala ngati bedi limene amagonapo pa nthawi ya kusamba kwake.+ Ndipo chinthu chilichonse chimene angakhalepo, chizikhala chodetsedwa mmene chingakhalire chodetsedwa pa nthawi ya kusamba kwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena