Machitidwe 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo anamunena kuti: “Wachita misala eti!” Koma iye analimbikira kunena motsimikiza kuti akunena zoona. Iwo tsopano anayamba kunena kuti: “Ndi mngelo wake ameneyo.”+ Aheberi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+
15 Iwo anamunena kuti: “Wachita misala eti!” Koma iye analimbikira kunena motsimikiza kuti akunena zoona. Iwo tsopano anayamba kunena kuti: “Ndi mngelo wake ameneyo.”+
14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+