Genesis 48:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki, apitirize kutchulidwa kudzela mwa anawa,+Komanso, anawa adzachulukane, adzakhale khamu la anthu padziko lapansi.”+ Mateyu 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Samalani anthu inu kuti musanyoze mmodzi wa tianati, chifukwa ndikukutsimikizirani kuti angelo awo+ kumwamba amaona nkhope ya Atate wanga wakumwamba nthawi zonse.+
16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki, apitirize kutchulidwa kudzela mwa anawa,+Komanso, anawa adzachulukane, adzakhale khamu la anthu padziko lapansi.”+
10 Samalani anthu inu kuti musanyoze mmodzi wa tianati, chifukwa ndikukutsimikizirani kuti angelo awo+ kumwamba amaona nkhope ya Atate wanga wakumwamba nthawi zonse.+