Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ine ndili nawe ndipo ndikuyang’anira pa ulendo wako wonse, kufikira ndidzakubwezera kumalo ano.+ Sindidzakusiya kufikira nditachitadi zimene ndanena kwa iwe.”+

  • Genesis 31:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako, mngelo wa Mulungu woona anandiitana m’malotowo kuti, ‘Yakobo!’ Ine ndinayankha kuti, ‘Ine pano.’+

  • Ekisodo 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwa kukoma mtima kwanu kosatha, mwatsogolera anthu amene munawawombola.+

      Mwa mphamvu yanu, inu mudzatengera anthu anu kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala.+

  • Yobu 19:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ineyo ndikudziwa bwino kuti wondiwombola+ ali moyo,

      Ndipo adzabwera pambuyo panga n’kuimirira+ pafumbi.

  • Salimo 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+

      Ndipo amawapulumutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena