Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu akafa, kodi angakhalenso ndi moyo?+

      Ndidzadikira masiku onse a ntchito yanga yokakamiza,+

      Mpaka mpumulo wanga utafika.+

  • Salimo 19:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+

      Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+

  • Salimo 69:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yandikirani moyo wanga ndi kuupulumutsa.+

      Ndiwomboleni kwa adani anga.+

  • Salimo 103:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+

      Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+

  • Miyambo 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti Wowawombola ndi wamphamvu, ndipo adzawateteza pa mlandu wawo ndi iwe.+

  • Mateyu 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena