Salimo 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova amawombola moyo wa atumiki ake.+Ndipo palibe aliyense wothawira kwa iye amene adzapezeka wolakwa.+ Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+ Salimo 69:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yandikirani moyo wanga ndi kuupulumutsa.+Ndiwomboleni kwa adani anga.+
22 Yehova amawombola moyo wa atumiki ake.+Ndipo palibe aliyense wothawira kwa iye amene adzapezeka wolakwa.+
13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+