Salimo 116:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti inu mwapulumutsa moyo wanga ku imfa,+Mwateteza maso anga kuti asakhetse misozi ndiponso phazi langa kuti lisapunthwe.+ 2 Akorinto 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anatipulumutsadi ku chinthu choopsa, ndicho imfa, ndipo adzatipulumutsabe.+ Tikukhulupirira kuti iye apitiriza kutipulumutsa.+
8 Pakuti inu mwapulumutsa moyo wanga ku imfa,+Mwateteza maso anga kuti asakhetse misozi ndiponso phazi langa kuti lisapunthwe.+
10 Iye anatipulumutsadi ku chinthu choopsa, ndicho imfa, ndipo adzatipulumutsabe.+ Tikukhulupirira kuti iye apitiriza kutipulumutsa.+