Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mukamuzunza ngakhale pang’ono, iye n’kundilirira, ndidzamva ndithu kulira kwake.+

  • Deuteronomo 27:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza+ chiweruzo+ cha mlendo wokhala pakati panu,+ mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)

  • Salimo 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.

      Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+

      Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.

      Inu mwakhala mthandizi wake.+

  • Salimo 68:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tate wa ana amasiye* ndi woweruzira akazi amasiye milandu,+

      Ndi Mulungu amene amakhala m’malo ake oyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena