Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iye amaperekera chiweruzo ana amasiye* ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo wokhala pakati panu+ moti amam’patsa mkate ndi chofunda.

  • Salimo 146:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+

      Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+

      Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+

  • Yeremiya 49:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Asiyeni ana anu amasiye.*+ Ine ndidzawasiya amoyo ndipo akazi anu amasiye adzandikhulupirira.”+

  • Hoseya 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+

  • Aheberi 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Moti tikhale olimba mtima ndithu+ ndipo tinene kuti: “Yehova* ndiye mthandizi wanga. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena