Levitiko 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala+ za m’munda mwanu, ndipo musamatole mphesa zimene zamwazika m’munda mwanu. Zimenezo muzisiyira wovutika ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Deuteronomo 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachitire chinyengo waganyu wovutika ndiponso wosauka n’kumubera, kaya akhale mmodzi wa abale ako kapena mmodzi mwa alendo okhala m’dziko lanu, amene ali m’mizinda yanu.+
10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala+ za m’munda mwanu, ndipo musamatole mphesa zimene zamwazika m’munda mwanu. Zimenezo muzisiyira wovutika ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
14 “Usachitire chinyengo waganyu wovutika ndiponso wosauka n’kumubera, kaya akhale mmodzi wa abale ako kapena mmodzi mwa alendo okhala m’dziko lanu, amene ali m’mizinda yanu.+