Levitiko 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala zamʼmunda mwanu kapena kutola mphesa zimene zamwazika mʼmunda mwanu. Zimenezo muzisiyira anthu osauka*+ ndi mlendo wokhala pakati panu. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala zamʼmunda mwanu kapena kutola mphesa zimene zamwazika mʼmunda mwanu. Zimenezo muzisiyira anthu osauka*+ ndi mlendo wokhala pakati panu. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.