Levitiko 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala+ za m’munda mwanu, ndipo musamatole mphesa zimene zamwazika m’munda mwanu. Zimenezo muzisiyira wovutika ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
10 Komanso, musamakolole mphesa zotsala+ za m’munda mwanu, ndipo musamatole mphesa zimene zamwazika m’munda mwanu. Zimenezo muzisiyira wovutika ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.