Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo inuyo, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, waganyu wanu, mlendo wokhaliratu amene akukhala pakati panu, ndi alendo ena okhala m’nyumba mwanu, muzidya zimene zamera m’chaka cha sabatacho.

  • Deuteronomo 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Wina mwa abale ako akasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, usamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lako.+

  • Rute 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Atatha kudya ananyamuka kukayambanso kukunkha.+ Tsopano Boazi analamula anyamata ake kuti: “Muloleni akunkhe pomwe mwadula kale balere, ndipo musam’vutitse.+

  • Salimo 140:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+

      Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena