Levitiko 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda mwanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Rute 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsiku lina Rute mkazi wachimowabu uja anapempha Naomi kuti: “Chonde ndiloleni ndipite kuminda ndikakunkhe+ balere m’mbuyo mwa aliyense amene angandikomere mtima.” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.”
9 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda mwanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+
2 Tsiku lina Rute mkazi wachimowabu uja anapempha Naomi kuti: “Chonde ndiloleni ndipite kuminda ndikakunkhe+ balere m’mbuyo mwa aliyense amene angandikomere mtima.” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.”