Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda mwanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+

  • Levitiko 23:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda m’dziko lanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wovutika+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”

  • Deuteronomo 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Ukaiwala mtolo wa tirigu pokolola m’munda wako,+ usabwerere kukatenga mtolowo. Uzisiyira mlendo wokhala m’dziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+ Uzichita zimenezi kuti Yehova Mulungu wako akudalitse pa chilichonse chimene dzanja lako likuchita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena