Levitiko 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda m’dziko lanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wovutika+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’” Rute 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, muzisololapo balere wina pamitolopo n’kumamusiya pansi kuti iye akunkhe.+ Ndipo musamuletse.” Salimo 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+
22 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda m’dziko lanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wovutika+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
16 Komanso, muzisololapo balere wina pamitolopo n’kumamusiya pansi kuti iye akunkhe.+ Ndipo musamuletse.”
41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+