Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda mwanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+

  • Deuteronomo 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Ukaiwala mtolo wa tirigu pokolola m’munda wako,+ usabwerere kukatenga mtolowo. Uzisiyira mlendo wokhala m’dziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+ Uzichita zimenezi kuti Yehova Mulungu wako akudalitse pa chilichonse chimene dzanja lako likuchita.+

  • Rute 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo Rute ananyamuka n’kupita, ndipo anakalowa m’munda wina ndi kuyamba kukunkha m’mbuyo mwa okolola.+ Mwamwayi mundawo unali wa Boazi,+ wa ku banja la Elimeleki.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena