Salimo 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa mwandiweruzira mlandu wanga ndi dandaulo langa.+Mwakhala pampando wachifumu ndipo mukuweruza mwachilungamo.+ Salimo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti muweruze mwana wamasiye komanso woponderezedwa.+Mudzatero kuti munthu wamba wochokera kufumbi asachititsenso anthu ena kunjenjemera.+ Salimo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti iye sananyoze,+Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+ Salimo 72:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.
4 Chifukwa mwandiweruzira mlandu wanga ndi dandaulo langa.+Mwakhala pampando wachifumu ndipo mukuweruza mwachilungamo.+
18 Kuti muweruze mwana wamasiye komanso woponderezedwa.+Mudzatero kuti munthu wamba wochokera kufumbi asachititsenso anthu ena kunjenjemera.+
24 Pakuti iye sananyoze,+Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+
4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.