Salimo 68:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tate wa ana amasiye* ndi woweruzira akazi amasiye milandu,+Ndi Mulungu amene amakhala m’malo ake oyera.+ Salimo 146:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+
5 Tate wa ana amasiye* ndi woweruzira akazi amasiye milandu,+Ndi Mulungu amene amakhala m’malo ake oyera.+
9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+
27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+