Yobu 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Madalitso+ a munthu amene watsala pang’ono kuwonongedwa ankabwera kwa ine,Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ 1 Timoteyo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Lemekeza akazi amasiye amene alidi amasiye.+
13 Madalitso+ a munthu amene watsala pang’ono kuwonongedwa ankabwera kwa ine,Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+
17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+