1 Timoteyo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati mkazi aliyense wokhulupirira ali ndi achibale amene ndi akazi amasiye, aziwathandiza,+ kuti akazi amasiyewo asakhale cholemetsa ku mpingo. Zikatero, mpingowo ungathe kuthandiza amene alidi akazi amasiye.+
16 Ngati mkazi aliyense wokhulupirira ali ndi achibale amene ndi akazi amasiye, aziwathandiza,+ kuti akazi amasiyewo asakhale cholemetsa ku mpingo. Zikatero, mpingowo ungathe kuthandiza amene alidi akazi amasiye.+