2 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘“Ndithu magazi+ a Naboti ndi magazi a ana ake+ amene ndawaona dzulo,” watero Yehova, “ndidzawabwezera+ pa iwe ndithu m’munda uwu,” Yehova watero.’ Choncho munyamule, umuponye m’mundamo mogwirizana ndi mawu a Yehova.”+ 2 Mbiri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+
26 ‘“Ndithu magazi+ a Naboti ndi magazi a ana ake+ amene ndawaona dzulo,” watero Yehova, “ndidzawabwezera+ pa iwe ndithu m’munda uwu,” Yehova watero.’ Choncho munyamule, umuponye m’mundamo mogwirizana ndi mawu a Yehova.”+
23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+