1 Mafumu 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wa m’banja la Ahabu wofera mumzinda, agalu adzamudya, ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.+
24 Munthu wa m’banja la Ahabu wofera mumzinda, agalu adzamudya, ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.+