1 Mafumu 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wa m’banja la Yerobowamu wofera mumzinda, agalu adzamudya,+ ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya,+ chifukwa choti Yehova wanena.”’ 1 Mafumu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu aliyense wa m’banja la Basa amene adzafere mumzinda, agalu adzamudya ndipo amene adzafere kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.”+ Yeremiya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ndidzawagwetsera masoka a mitundu inayi,’+ watero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, zolengedwa zouluka zam’mlengalenga+ ndi zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga. Chivumbulutso 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 kuti mudzadye minofu+ ya mafumu, ya akuluakulu a asilikali, ya amuna amphamvu,+ ya mahatchi+ ndi ya okwerapo ake, ndi minofu ya onse, ya mfulu ndi ya akapolo, ya olemekezeka ndi ya onyozeka.”
11 Munthu wa m’banja la Yerobowamu wofera mumzinda, agalu adzamudya,+ ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya,+ chifukwa choti Yehova wanena.”’
4 Munthu aliyense wa m’banja la Basa amene adzafere mumzinda, agalu adzamudya ndipo amene adzafere kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.”+
3 “‘Ndidzawagwetsera masoka a mitundu inayi,’+ watero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, zolengedwa zouluka zam’mlengalenga+ ndi zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.
18 kuti mudzadye minofu+ ya mafumu, ya akuluakulu a asilikali, ya amuna amphamvu,+ ya mahatchi+ ndi ya okwerapo ake, ndi minofu ya onse, ya mfulu ndi ya akapolo, ya olemekezeka ndi ya onyozeka.”