1 Mafumu 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wa m’banja la Yerobowamu wofera mumzinda, agalu adzamudya,+ ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya,+ chifukwa choti Yehova wanena.”’ Yobu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zoipa zimene munthu anachita, Mulungu adzazisungira ana ake omwe,+Adzam’patsa mphoto yake, ndipo iye adzaidziwa.+
11 Munthu wa m’banja la Yerobowamu wofera mumzinda, agalu adzamudya,+ ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya,+ chifukwa choti Yehova wanena.”’
19 Zoipa zimene munthu anachita, Mulungu adzazisungira ana ake omwe,+Adzam’patsa mphoto yake, ndipo iye adzaidziwa.+