1 Mafumu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu aliyense wa m’banja la Basa amene adzafere mumzinda, agalu adzamudya ndipo amene adzafere kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.”+ 1 Mafumu 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wa m’banja la Ahabu wofera mumzinda, agalu adzamudya, ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.+
4 Munthu aliyense wa m’banja la Basa amene adzafere mumzinda, agalu adzamudya ndipo amene adzafere kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.”+
24 Munthu wa m’banja la Ahabu wofera mumzinda, agalu adzamudya, ndipo wofera kuthengo, mbalame zam’mlengalenga zidzamudya.+